Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 38:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo anapanga zokowera za mizati nsanamira ndi nsichi ndi masekeli aja chikwi chimodzi kudza mazana asanu ndi awiri mphambu asanu, nakuta mitu yake, nazigwirizanitsa pamodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo anapanga zokowera za mizati nsanamira ndi nsichi ndi masekeli aja chikwi chimodzi kudza mazana asanu ndi awiri mphambu asanu, nakuta mitu yake, nazigwirizitsana pamodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Ndi makilogaramu otsalawo adapanga ngoŵe za pa nsanamirazo ndipo adakuta nsonga za nsanamira ndi kupanga mitanda yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Makilogalamu otsalawo anagwiritsa ntchito popanga ngowe zamzati kukutira pamwamba pa mizati ndiponso kupanga zingwe zake.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 38:28
3 Mawu Ofanana  

Nsichi zonse za pabwalo pozungulira zimangike pamodzi ndi mitanda yasiliva; zokowera zao zasiliva, ndi makamwa ao amkuwa.


Ndipo matalente zana limodzi a siliva ndiwo a kuyengera makamwa a malo opatulika, ndi makamwa a nsalu yotchinga; makamwa zana limodzi matalente zana limodzi, talente limodzi kamwa limodzi.


Ndi mkuwa wa choperekacho ndiwo matalente makumi asanu ndi awiri, ndi masekeli zikwi ziwiri kudza mazana anai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa