Eksodo 38:29 - Buku Lopatulika29 Ndi mkuwa wa choperekacho ndiwo matalente makumi asanu ndi awiri, ndi masekeli zikwi ziwiri kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndi mkuwa wa choperekacho ndiwo matalente makumi asanu ndi awiri, ndi masekeli zikwi ziwiri kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Mkuŵa umene adaapereka kwa Chauta udakwana makilogaramu 2,425 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mkuwa ochokera ku nsembe yoweyula unali makilogalamu 2,425. Onani mutuwo |