Eksodo 38:15 - Buku Lopatulika15 momwemonso pa mbali ina: pa mbali ino ndi pa mbali ina ya chipata cha pabwalo panali nsalu zotchingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 momwemonso pa mbali ina: pa mbali yino ndi pa mbali ina ya chipata cha pabwalo panali nsalu zochingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pa mbali inayo panali chimodzimodzi. Choncho pa mbali zonse ziŵirizo za chipata choloŵera ku bwalo chija, panali nsalu zochinga, zotalika mamita asanu ndi aŵiri, zokhala ndi nsanamira zitatu ndi masinde atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 polowera mʼbwalo panali nsalu yotchinga ya mamita asanu ndi awiri pamodzi ndi mizati itatu ndi matsinde atatu. Onani mutuwo |