Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 38:16 - Buku Lopatulika

16 Nsalu zotchingira zonse za pabwalo pozungulira zinali za bafuta wa thonje losansitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Nsalu zochingira zonse za pabwalo pozungulira zinali za bafuta wa thonje losansitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Nsalu zonse zochinga kuzungulira bwalolo zinali za bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Katani yonse yotchinga kuzungulira chihema inali yofewa, yosalala ndi yolukidwa bwino.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 38:16
2 Mawu Ofanana  

momwemonso pa mbali ina: pa mbali ino ndi pa mbali ina ya chipata cha pabwalo panali nsalu zotchingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu.


Ndipo makamwa a nsichi anali amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zasiliva; ndi zokutira mitu yake zasiliva; ndi nsichi zonse za pabwalo zinagwirana pamodzi ndi siliva.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa