Eksodo 38:14 - Buku Lopatulika14 Nsalu zotchingira za pa mbali imodzi ya chipata nza mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Nsalu zochingira za pa mbali imodzi ya chipata nza mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Panali nsalu zochinga pa mbali imodzi ya chipata, zotalika mamita asanu ndi aŵiri, zokhala ndi nsanamira zake zitatu ndi masinde atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mbali imodzi yachipata kunali nsalu yotchinga yotalika mamita asanu ndi awiri, mizati itatu ndi matsinde atatu, Onani mutuwo |