Eksodo 38:13 - Buku Lopatulika13 Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pa mbali inayo yakuvuma panalinso mamita 23. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, inalinso yotalika mamita 23. Onani mutuwo |