Eksodo 37:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo akerubi anafunyulira mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba chotetezerapo ndi mapiko ao, ndi nkhope zao zopenyana; zinapenya kuchotetezerapo nkhope zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo akerubi anafunyulira mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba chotetezerapo ndi mapiko ao, ndi nkhope zao zopenyana; zinapenya kuchotetezerapo nkhope zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mapiko a akerubiwo adaŵatambalitsa pamwamba, kuphimba chivundikiro chija. Adakhala choyang'anana, ndipo aliyense anali kuyang'anananso ndi chivundikirocho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mapiko a Akerubiwo anatambasukira pamwamba pa chivundikiro cha bokosilo kuti achiphimbe. Akerubiwo anakhala choyangʼanana, aliyense kuyangʼana chivundikirocho. Onani mutuwo |