Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 37:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo anapanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anapanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Bezalele adapanganso tebulo la matabwa a mtengo wa kasiya, m'litali mwake masentimita 91, muufupi mwake masentimita 46, ndipo mumsinkhu mwake masentimita 69,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Iwo anapanga tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 37:10
13 Mawu Ofanana  

Ndipo Solomoni anapanga zipangizo zonse za m'nyumba ya Yehova: guwa la nsembe lagolide, ndi gome lagolide loikapo mikate yoonekera;


ndi gomelo ndi zipangizo zake, ndi choikaponyali choona ndi zipangizo zake, ndi guwa la nsembe lofukizapo;


gome, ndi mphiko zake, ndi zipangizo zake zonse, ndi mkate woonekera;


ndipo analikuta ndi golide woona, nalipangira mkombero wagolide pozungulira pake.


Ndipo akerubi anafunyulira mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba chotetezerapo ndi mapiko ao, ndi nkhope zao zopenyana; zinapenya kuchotetezerapo nkhope zao.


Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikaponyalicho, ndi kuyatsa nyali zake.


Koma inu muliipsa, pakunena inu, Gome la Ambuye laipsidwa, ndi zipatso zake, chakudya chake, chonyozeka.


Ndipo Mau anasandulika thupi, nakhazikika pakati pa ife, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wonga wa wobadwa yekha wa Atate, wodzala ndi chisomo ndi choonadi.


Chifukwa mwa kudzala kwake tinalandira ife tonse, chisomo chosinthana ndi chisomo.


kwa iwo amene Mulungu anafuna kuwazindikiritsa ichi chimene chili chuma cha ulemerero wa chinsinsi pakati pa amitundu, ndiye Khristu mwa inu, chiyembekezo cha ulemerero;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa