Eksodo 37:11 - Buku Lopatulika11 ndipo analikuta ndi golide woona, nalipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo analikuta ndi golide woona, nalipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono adalikuta ndi golide wabwino kwambiri, nalemba mkombelo wagolide kuzungulira tebulo lonselo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka analikuta ndi golide wabwino kwambiri, ndipo anapanga mkombero wagolide mʼmbali mwake. Onani mutuwo |