Eksodo 37:12 - Buku Lopatulika12 Analipangiranso mitanda pozungulirapo, yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira anapangirapo mkombero wagolide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Analipangiranso mitanda pozungulirapo, yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira anapangirapo mkombero wagolide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adapanga fulemu lagolide pozungulira, muufupi mwake munali ngati kuyesa chikhatho, nalemba mkombero wagolide molizungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwo anapanga feremu yozungulira tebulo, mulifupi mwake ngati chikhatho cha dzanja, ndipo anayika mkombero wagolide kuzungulira feremuyo. Onani mutuwo |