Eksodo 37:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo analiyengera mphete zinai zagolide, naika mphetezo pangodya zake zinai zokhala pa miyendo yake inai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo analiyengera mphete zinai zagolide, naika mphetezo pangodya zake zinai zokhala pa miyendo yake inai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Kenaka adapanganso mphete zinai zagolide za tebulolo, naziika pa ngodya zinai ku miyendo ya tebulolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iwo anapanga mphete zinayi zagolide ndipo anazilumikiza ku ngodya zake zinayi, kumene kunali miyendo yake inayi. Onani mutuwo |