Eksodo 37:14 - Buku Lopatulika14 Mphetezo zinali pafupi pa mitanda, zikhale zopisamo mphiko kunyamulira nazo gomelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Mphetezo zinali pafupi pa mitanda, zikhale zopisamo mphiko kunyamulira nazo gomelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Mphete zopisiramo mphiko ponyamula tebulolo, zinali pafupi ndi fulemu lija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mphetezo anaziyika kufupi ndi feremu kuti azikolowekamo nsichi zonyamulira tebuloyo. Onani mutuwo |