Eksodo 37:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide, kunyamulira nazo gomelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide, kunyamulira nazo gomelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Adapanga mphiko za matabwa a mtengo wa kasiya, nazikuta ndi golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide kuti azinyamulira tebulolo. Onani mutuwo |