Eksodo 37:8 - Buku Lopatulika8 kerubi mmodzi pa mbali yake imodzi, ndi kerubi wina pa mbali yake ina; anapanga akerubi ochokera m'chotetezerapo, pa mathungo ake awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 kerubi mmodzi pa mbali yake imodzi, ndi kerubi wina pa mbali yake ina; anapanga akerubi ochokera m'chotetezerapo, pa mathungo ake awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 wina uku wina uku. Adaŵapangira kumodzi ndi chivundikirocho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye anapanga kerubi mmodzi mbali ina ndi wina mbali inayo. Akerubiwa anawapangira limodzi ndi chivundikirocho mʼmapeto mwa mbali ziwirizo. Onani mutuwo |