Eksodo 37:7 - Buku Lopatulika7 Anapanganso akerubi awiri agolide; anachita kuwasula mapangidwe ake, pa mathungo ake awiri a chotetezerapo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Anapanganso akerubi awiri agolide; anachita kuwasula mapangidwe ake, pa mathungo ake awiri a chotetezerapo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pa nsonga zake ziŵiri za chivundikirocho, adazokotapo akerubi aŵiri a golide wosula ndi nyundo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo anapanga Akerubi awiri agolide osula ndi nyundo ndi kuwayika mbali ziwiri za chivundikirocho. Onani mutuwo |