Eksodo 37:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anapanga chotetezerapo cha golide woona; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anapanga chotetezerapo cha golide woona; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kenaka adapanga chivundikiro cha golide wabwino kwambiri, kutalika kwake masentimita 114, muufupi wake masentimita 69. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye anapanga chivundikiro cha bokosilo cha golide wabwino kwambiri, kutalika kwake masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69. Onani mutuwo |