Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 37:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo anapisa mphiko m'mphetezo pa mbali zake za likasalo, kuti anyamulire nazo likasa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo anapisa mphiko m'mphetezo pa mbali zake za likasalo, kuti anyamulire nazo likasa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 ndipo mphikozo adazipisa m'mphete zija pa mbali zonse ziŵiri za bokosilo, kuti azinyamulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndipo analowetsa nsichizo mʼmphete zija za mbali zonse ziwiri za bokosilo kuti azinyamulira.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 37:5
6 Mawu Ofanana  

Ndipo mphikozo zinatalika kuti nsonga za mphiko zidaoneka ku malo opatulika chakuno cha chipinda chamkati; koma sizinaoneke kubwalo; ndipo zikhala pomwepo mpaka lero lino.


Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide.


Ndipo anapanga chotetezerapo cha golide woona; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu.


koma iwe, uike Alevi asunge chihema cha mboni, ndi zipangizo zake zonse, ndi zonse ali nazo; azinyamula chihema, ndi zipangizo zake zonse; namtumikire, namange mahema ao pozungulira pa chihema.


Atatha Aroni ndi ana ake aamuna kuphimba malo opatulika, ndi zipangizo zake zonse za malo opatulika, pofuna kumuka am'chigono; atatero, ana a Kohati adze kuzinyamula; koma asakhudze zopatulikazo, kuti angafe. Zinthu izi ndizo akatundu a ana a Kohati m'chihema chokomanako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa