Eksodo 37:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adapanga mphiko zinai za matabwa a mtengo wa kasiya, nazikuta ndi golide, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kenaka anapanga mizati yamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide. Onani mutuwo |