Eksodo 37:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo anazipanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo anazipanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Mphikozo adazipanga ndi matabwa a mtengo wa kasiya, naikuta ndi golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Anapanga mizati yamtengo wa mkesha ndipo anayikuta ndi golide. Onani mutuwo |