Eksodo 37:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo analipangira mphete ziwiri zagolide pansi pa mkombero wake, pangodya zake ziwiri, pa mbali zake ziwiri, zikhale zopisamo mphiko kulinyamulira nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo analipangira mphete ziwiri zagolide pansi pa mkombero wake, pangodya zake ziwiri, pa mbali zake ziwiri, zikhale zopisamo mphiko kulinyamulira nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Adapanga mphete ziŵiri zagolide zonyamulira guwalo, ndipo adazilumikiza ku mbali zonse ziŵiri za guwa, pansi pa mkombero uja, kuti apisemo mphiko zonyamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Anapanga mphete ziwiri pansi pa mkomberowo ndi kulumikiza ku mbali zonse ziwiri kuti apisemo nsichi zonyamulira. Onani mutuwo |