Eksodo 37:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anapanga guwa la nsembe lofukizapo la mtengo wakasiya; utali wake mkono, ndi kupingasa kwake mkono, laphwamphwa; ndi msinkhu wake mikono iwiri; nyanga zake zinatuluka m'mwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anapanga guwa la nsembe lofukizapo la mtengo wakasiya; utali wake mkono, ndi kupingasa kwake mkono, laphwamphwa; ndi msinkhu wake mikono iwiri; nyanga zake zinatuluka m'mwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Guwa lofukizirapo lubani adalipanga ndi matabwa a mtengo wa kasiya. Linali lalibanda, muutalika mwake munali masentimita 46, muufupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 91, ndipo nyanga zake zidapangidwira kumodzi ndi guwalo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iwo anapanga guwa lamatabwa amtengo wa mkesha lofukizirapo lubani. Linali lofanana mbali zonse, mulitali masentimita 46, mulifupi masentimita 46, ndipo msinkhu masentimita 91, ndipo nyanga zake zinapangidwa kumodzi ndi guwalo. Onani mutuwo |