Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 37:24 - Buku Lopatulika

24 Anachipanga ichi ndi zipangizo zake zonse za talente wa golide woona.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Anachipanga ichi ndi zipangizo zake zonse za talente wa golide woona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Popanga choikaponyalecho, pamodzi ndi zipangizo zake zonsezo, adagwiritsa ntchito makilogaramu 34 a golide wabwino kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Iwo anapanga choyikapo nyale ndi zipangizo zake zonse zagolide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 37:24
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anapanga nyali zake zisanu ndi ziwiri ndi mbano zake, ndi zoolera zake, za golide woona.


Ndipo anapanga guwa la nsembe lofukizapo la mtengo wakasiya; utali wake mkono, ndi kupingasa kwake mkono, laphwamphwa; ndi msinkhu wake mikono iwiri; nyanga zake zinatuluka m'mwemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa