Eksodo 37:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo anapanga nyali zake zisanu ndi ziwiri ndi mbano zake, ndi zoolera zake, za golide woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo anapanga nyali zake zisanu ndi ziwiri ndi mbano zake, ndi zoolera zake, za golide woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndipo adapanga nyale zisanu ndi ziŵiri za pa choikaponyalecho, napanganso mbanira ndiponso zoolera phulusa za golide wabwino kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iwo anapanga nyale zisanu ndi ziwiri, mbaniro ndi zowolera phulusa, zonse zinali zagolide wabwino kwambiri. Onani mutuwo |