Eksodo 37:22 - Buku Lopatulika22 Mitu yao ndi mphanda zao zinatuluka m'mwemo; chonsechi chinali chosulika pamodzi cha golide woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Mitu yao ndi mphanda zao zinatuluka m'mwemo; chonsechi chinali chosulika pamodzi cha golide woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Nkhunjezo, pamodzi ndi nthambizo, zidapangidwira kumodzi ndi choikaponyale chija. Chonsecho chinali chinthu chimodzi chagolide, chosula ndi nyundo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Mphukira ndi nthambi zonse zinasulidwa kumodzi ndi choyikapo nyalecho ndi golide wabwino kwambiri. Onani mutuwo |