Eksodo 37:2 - Buku Lopatulika2 ndipo analikuta ndi golide woona m'kati ndi kunja, nalipangira mkombero wa golide pozungulira pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo analikuta ndi golide woona m'kati ndi kunja, nalipangira mkombero wa golide pozungulira pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono lonselo adalikuta ndi golide m'kati mwake ndi kunja komwe, ndipo adalemba mkombero wagolide kuzungulira bokosi lonselo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye analikuta bokosilo ndi golide wabwino kwambiri mʼkati mwake ndi kunja komwe. Anapanganso mkombero wagolide kuzungulira bokosilo. Onani mutuwo |