Eksodo 37:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Bezalele anapanga likasa la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Bezalele anapanga likasa la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Bezalele adapanga bokosi lachipangano ndi matabwa a mtengo wa kasiya. Kutalika kwake kunali masentimita 114, muufupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Bezaleli anapanga Bokosi la Chipangano lamatabwa amtengo wa mkesha. Kutalika kwake kunali masentimita 114, mulifupi mwake munali masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwo |