Eksodo 36:38 - Buku Lopatulika38 ndi nsanamira zake zisanu ndi zokowera zao; nakuta mitu yao ndi mitanda yao ndi golide; ndi makamwa ao asanu anali amkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 ndi nsanamira zake zisanu ndi zokowera zao; nakuta mitu yao ndi mitanda yao ndi golide; ndi makamwa ao asanu anali amkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Tsono adapanga nsanamira zisanu zokhala ndi ngoŵe zokoŵera nsaluyo, ndipo mitu yake ndi mitanda yake adaikuta ndi golide, koma masinde ake anali amkuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Anapanga nsanamira zisanu ndi ngowe zake. Anakuta pamwamba pa nsanamirazo ndi zomangira zake ndi golide, ndipo anapanganso matsinde asanu amkuwa. Onani mutuwo |