Eksodo 37:18 - Buku Lopatulika18 ndi m'mbali zake munatuluka mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikaponyali zotuluka m'mbali yake imodzi, ndi mphanda zitatu za choikaponyali zotuluka m'mbali yake ina; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndi m'mbali zake munatuluka mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikapo nyali zotuluka m'mbali yake imodzi, ndi mphanda zitatu za choikapo nyali zotuluka m'mbali yake ina; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pa mbali zake adapanga nthambi zisanu ndi imodzi, zitatu pa mbali iliyonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mʼmbali mwake munali mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu mbali iliyonse. Onani mutuwo |