Eksodo 36:9 - Buku Lopatulika9 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi mikono inai; nsalu zonse zinafanana muyeso wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi mikono inai; nsalu zonse zinafanana muyeso wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 M'litali mwa nsalu iliyonse munali mamita 13, ndipo muufupi mwake munali masentimita 183. Zonsezo zinali zofanana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Nsalu zonse zinali zofanana. Mulitali mwake zinali mamita khumi ndi atatu, mulifupi mamita awiri. Onani mutuwo |