Eksodo 36:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo anaipangira mizati inai ya kasiya, nazikuta ndi golide; zokowera zao zinali zagolide; ndipo anaziyengera makamwa anai asiliva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo anaipangira mizati inai ya kasiya, nazikuta ndi golide; zokowera zao zinali zagolide; ndipo anaziyengera makamwa anai asiliva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Adapanga nsanamira zinai zakasiya zogwirizira nsalu yochingira ija. Nsanamirazo zinali zitakutidwa ndi golide, ndipo adaika ngoŵe zokoŵera ku nsanamirazo. Adapanga masinde anai asiliva ogwirizira nsanamirazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Iwo anapanga nsanamira zinayi zamtengo wa mkesha zokutidwa ndi golide. Anapanganso ngowe zagolide za nsanamirazo ndi matsinde asiliva anayi. Onani mutuwo |