Eksodo 36:37 - Buku Lopatulika37 Ndipo anaomba nsalu yotsekera pa khomo la chihemacho, ya lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya wopikula; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndipo anaomba nsalu yotsekera pa khomo la chihemacho, ya lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya wopikula; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Pa chipata choloŵera m'chihemamo, adaikapo nsalu yochinga yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndiponso nsalu ya bafuta wosalala, wopikidwa bwino ndi wopetedwa mwaluso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Anapanga nsalu ya pa chipata cholowera mu chihema, yamtundu wamtambo, wapepo ndi ofiira yomwe inali yofewa ndi yosalala, yopetedwa bwino ndi amisiri aluso. Onani mutuwo |