Eksodo 36:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo anakuta matabwa ndi golide, napanga mphete zao zagolide zikhale zopisamo mitandayo, nakuta mitandayo ndi golide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo anakuta matabwa ndi golide, napanga mphete zao zagolide zikhale zopisamo mitandayo, nakuta mitandayo ndi golide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Mafulemu onsewo adaŵakuta ndi golide, ndipo adamangapo mphete zagolide zopisiramo mitanda ija, imene adaikutanso ndi golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Iwo anakuta maferemuwo ndi golide ndiponso anapanga mphete zagolide zogwiriziza mitandayo. Ndipo mitandayonso anayikuta ndi golide. Onani mutuwo |