Eksodo 36:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo anapititsa mtanda wa pakatipo, pakati pa matabwa kufikira kuthungo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo anapititsa mtanda wa pakatipo, pakati pa matabwa kufikira kuthungo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Tsono adapanga mtanda wapakati chapakatimpakati, wogwira mafulemuwo kuyambira ku mbali imodzi ya chihema mpaka mbali ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Anapanga mtanda wapakati omwe umachokera pa maferemu a mbali ina mpaka mbali inanso. Onani mutuwo |