Eksodo 36:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anapanga mitanda ya mtengo wakasiya; isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anapanga mitanda ya mtengo wakasiya; isanu ya matabwa a pa mbali ina ya Kachisi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Kenaka adapanga mitanda ya matabwa a mtengo wa kasiya, isanu ya mafulemu a mbali imodzi ya chihema, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Iwo anapanganso mitanda ya matabwa amtengo wa mkesha. Mitanda isanu inali ya maferemu a mbali imodzi ya chihema, Onani mutuwo |