Eksodo 36:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo panali matabwa asanu ndi atatu. Ndi makamwa ao asiliva, makamwa khumi kudza asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo panali matabwa asanu ndi atatu. Ndi makamwa ao asiliva, makamwa khumi kudza asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Motero panali mafulemu asanu ndi atatu, ndi masinde asiliva 16, aŵiri pansi pa fulemu lililonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Choncho panali maferemu asanu ndi atatu ndiponso matsinde 16 asiliva, awiri anali pansi pa feremu iliyonse. Onani mutuwo |