Eksodo 36:32 - Buku Lopatulika32 ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzake ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a chihema ali pa mbali ya kumadzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzake ya Kachisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a Kachisi ali pa mbali ya kumadzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 isanu ya mafulemu a mbali inayo, ndiponso isanu ya mafulemu a mbali yakuzambwe, kumbuyo kwake kwa chihema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 mitanda isanu inanso inali ya maferemu a mbali inayo ndipo mitanda ina isanu ya mbali yakumadzulo, kumapeto kwenikweni kwa chihema. Onani mutuwo |