Eksodo 36:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo analandira kwa Mose chopereka chonse, chimene ana a Israele adabwera nacho chikhale cha machitidwe a ntchito ya malo opatulika, aipange nacho. Koma anaonjeza kubwera nazo kwa iye zopereka zaufulu, m'mawa ndi m'mawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo analandira kwa Mose chopereka chonse, chimene ana a Israele adabwera nacho chikhale cha machitidwe a ntchito ya malo opatulika, aipange nacho. Koma anaonjeza kubwera nazo kwa iye zopereka zaufulu, m'mawa ndi m'mawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndipo Mose adaŵapatsa zopereka zonse zaufulu zomangira malo opatulika zimene Aisraele adabwera nazo. Koma Aisraelewo ankapatsabe Mose zopereka zao m'maŵa mulimonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwo analandira kuchokera kwa Mose zopereka zonse Aisraeli anabweretsa kuti agwirire ntchito yomanga malo wopatulika. Ndipo anthu anapitirira kupereka zopereka zaufulu mmawa uliwonse. Onani mutuwo |