Eksodo 36:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo aluso onse, akuchita ntchito yonse ya malo opatulika, anadza onse ndi kusiya ntchito yao analinkuchita; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo aluso onse, akuchita ntchito yonse ya malo opatulika, anadza onse ndi kusiya ntchito yao analinkuchita; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono aluso onse amene ankagwira ntchito zomanga malo opatulika aja, aliyense potsata luso lake, adasiya ntchito zao, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kotero amisiri onse amene amagwira ntchito yonse ya malo wopatulika anasiya ntchitoyo Onani mutuwo |