Eksodo 36:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Mose adaitana Bezalele ndi Oholiyabu, ndi anthu onse aluso, amene Yehova adaika luso m'mtima mwao, onse ofulumidwa mtima ayandikize kuntchito kuichita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Mose adaitana Bezalele ndi Oholiyabu, ndi anthu onse aluso, amene Yehova adaika luso m'mtima mwao, onse ofulumidwa mtima ayandikize kuntchito kuichita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pamenepo Mose adaitana Bezalele, Oholiyabu ndi onse aluso amene Chauta adaŵapatsa nzeru, ndiponso onse amene anali okonzeka kuthandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo Mose anayitana Bezaleli ndi Oholiabu ndiponso munthu aliyense waluso amene Yehova anamupatsa luso ndiponso amene anali ndi mtima wofuna kugwira ntchito. Onani mutuwo |