Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:22 - Buku Lopatulika

22 Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a Kachisi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Thabwa lililonse linali ndi zolumikizira ziŵiri, ndipo mafulemu onse adaŵapanga ndi zolumikizira ziŵiri. Mafulemu onse adaŵapanga ndi zolumikizira zotere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Thabwa lililonse linali ndi zolumikizira ziwiri. Iwo anapanga maferemu onse a chihemacho ndi matabwa otere.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:22
3 Mawu Ofanana  

Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a chihema.


Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.


Ndipo anapanga matabwa a chihema; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa