Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo anapanga matabwa a chihema; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo anapanga matabwa a Kachisi; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Pa mbali yakumwera adapanga mafulemu makumi aŵiri,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Anapanga maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:23
2 Mawu Ofanana  

Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.


napanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa