Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:21 - Buku Lopatulika

21 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 M'litali mwa fulemu lililonse munali mamita anai ndi theka, ndipo muufupi mwake munali masentimita 69.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Feremu iliyonse inali yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake munali masentimita 69.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:21
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anapanga matabwa a chihema, oimirika, a mtengo wakasiya.


Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa