Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo anapanga matabwa a chihema, oimirika, a mtengo wakasiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo anapanga matabwa a Kachisi, oimirika, a mtengo wakasiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pambuyo pake adapanga mafulemu a chihemacho ndi matabwa a mtengo wa kasiya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Iwo anapanga maferemu amatabwa amtengo wa mkesha oyimikira chihemacho.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:20
8 Mawu Ofanana  

Ndipo azipanga likasa la mtengo wakasiya: utali wake mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwake mkono ndi hafu, msinkhu wake mkono ndi hafu.


ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;


Ndipo anasokera hemalo chophimba cha zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu pamwamba pake.


Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.


Ndipo Israele anakhala mu Sitimu, ndipo anthu anayamba kuchita chigololo ndi ana aakazi a Mowabu;


Potero ndinapanga likasa la mtengo wakasiya, ndinasemanso magome awiri amiyala onga oyamba aja, ndi kukwera m'phirimo, magome awiri ali m'manja mwanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa