Eksodo 36:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anasokera hemalo chophimba cha zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu pamwamba pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anasokera hemalo chophimba cha zikopa za nkhosa zamphongo zonika zofiira, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu pamwamba pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndipo adapanga chophimbira china chofiira cha zikopa za nkhosa zamphongo. Potsiriza adapanganso chophimbira china cha zikopa zofeŵa, nkuchiika pamwamba pa zophimba zina zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo anapanga chikopa cha nkhosa zazimuna cha utoto wofiira chophimbira tentiyo ndipo pamwamba pake anapanganso chophimbira china cha zikopa za akatumbu. Onani mutuwo |