Eksodo 36:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anapanga zokowera makumi asanu zamkuwa kumanga pamodzi hemalo, kuti likhale limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anapanga zokowera makumi asanu zamkuwa kumanga pamodzi hemalo, kuti likhale limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Kenaka adapanga ngoŵe zokoŵera zokwanira makumi asanu zamkuŵa zolumikizira pamodzi nsalu ziŵirizo, kuti apange chinsalu chimodzi chophimbira chihema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo anapanga ngowe 50 zamkuwa zolowetsa mu zokolowekazo ndipo anaphatikiza nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi. Onani mutuwo |