Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu imodzi, ya kuthungo, ya chilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu ya kuthungo, ya chilumikizano china.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu imodzi, ya kuthungo, ya chilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu ya kuthungo, ya chilumikizano china.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Adasokanso magonga makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu yomalizira ya chinsalu choyambacho, ndi magonga ena makumi asanu m'mphepete mwa chinsalu chinacho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Kenaka anasokerera zokolowekamo makumi asanu mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsirizira ya nsalu yoyamba yolumikiza ija ndiponso anapanga zokolowekamo zina makumi asanu mʼmphepete mwa nsalu yotsirizira ya nsalu inanso yolumikiza ija.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:17
4 Mawu Ofanana  

Ndipo uziika magango a nsalu ya madzi m'mphepete mwake mwa nsalu imodzi, ku mkawo wa chilumikizano; nuchite momwemo m'mphepete mwake mwa nsalu ya kuthungo ya chilumikizano china.


Upangenso bwalo la chihema; pa mbali yake ya kumwera, kumwera, pakhale nsalu zotchingira za kubwalo za nsalu yabafuta wa thonje losansitsa, utali wake wa pa mbali imodzi mikono zana;


Ndipo anamanga pamodzi nsalu zisanu pazokha, ndi nsalu zisanu ndi imodzi pazokha.


Ndipo anapanga zokowera makumi asanu zamkuwa kumanga pamodzi hemalo, kuti likhale limodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa