Eksodo 36:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anamanga pamodzi nsalu zisanu pazokha, ndi nsalu zisanu ndi imodzi pazokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anamanga pamodzi nsalu zisanu pa zokha, ndi nsalu zisanu ndi imodzi pa zokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono adasokerera nsalu zisanu nkukhala chinsalu chimodzi, ndipo nsalu zinazo zisanu ndi imodzi, adazisokereranso kuti zikhale chinsalu chimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iwo analumikiza nsalu zisanu kukhala nsalu imodzi ndipo nsalu zinazo zisanu ndi imodzi, analumikizanso kukhala nsalu imodzinso. Onani mutuwo |