Eksodo 36:15 - Buku Lopatulika15 Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 M'litali mwa nsalu iliyonse munali mamita 14, ndipo muufupi mwake munali masentimita 183. Zonsezo zinali zofanana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Nsalu zonse khumi ndi imodzi zinali zofanana. Mulitali mwake munali mamita khumi ndi anayi ndipo mulifupi mwake munali mamita awiri. Onani mutuwo |