Eksodo 36:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anaomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale chophimba pamwamba pa chihema; anaomba nsalu zophimba khumi ndi imodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anaomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale hema pamwamba pa Kachisi; anaomba nsalu zophimba khumi ndi imodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pambuyo pake adasoka nsalu khumi ndi imodzi za ubweya wambuzi, napanga chophimbira pamwamba pa chihemacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iwo anapanga nsalu za ubweya wambuzi zophimba pamwamba pa chihemacho. Nsalu zonse pamodzi zinalipo khumi ndi imodzi. Onani mutuwo |