Eksodo 36:12 - Buku Lopatulika12 Anaika magango makumi asanu pansalu imodzi, naikanso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; magango anakomanizana lina ndi linzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Anaika magango makumi asanu pa nsalu imodzi, naikanso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; magango anakomanizana lina ndi linzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adasoka magonga makumi asanu pa chinsalu choyambacho, ndi magonga ena makumi asanu pa chinsalu chinacho, mopenyana ndi magonga a chinsalu choyamba aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwo anasokerera zokolowekamo makumi asanu pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Anapanga kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana. Onani mutuwo |